Mateyu 27:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene mkuru wa asilikari, ndi iwo anali naye 11 akudikira Yesu, anaona cibvomezi, ndi zinthu zimene zinacitidwa, anaopa kwambiri, nanena, Indedi Uyo ndiye Mwana wa Mulungu.

Mateyu 27

Mateyu 27:50-60