Mateyu 27:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo poyandikira ora lacisanu ndi cinai, Yesu 7 anapfuula ndi mau akuru, kunena, Eli, Eli, lama sabakitani? ndiko kunena kuti, Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji Ine?

Mateyu 27

Mateyu 27:39-51