Mateyu 27:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yudase yemwe anampereka Iye, poona kuti Iye anatsutsidwa kuti afe, analapa, nabweza ndalama zija zasiliva makumi atatu kwa ansembe akuru ndi akuru,

Mateyu 27

Mateyu 27:1-13