Mateyu 27:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analuka korona waminga, nambveka pamutu pace, namgwiritsa bango m'dzanja lamanja lace; ndipo anagwada pansi pamaso pace, namcitira cipongwe, nati, Tikuoneni, Mfumu ya Ayuda!

Mateyu 27

Mateyu 27:23-37