Mateyu 27:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kazembe anati kwa iwo, Mufuna kuti ndikumasulireni uti wa awa awiri? Ndipo iwo anati, Baraba.

Mateyu 27

Mateyu 27:16-27