Mateyu 27:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Pilato analikukhala pa mpando wakuweruza, mkazi wace anatumiza mau kwa iye, kunena, Musacite kanthu ndi munthu wolungamayo; pakuti lero m'kulota ine ndasauka kwambiri cifukwa ca Iye.

Mateyu 27

Mateyu 27:17-27