Mateyu 26:66-68 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

66. muganiza bwanji? lwo anayankha nati, 7 Ali woyenera kumupha,

67. 8 Pomwepo iwo anathira malobvu pankhope pace, nambwanyula Iye; ndipo ena anampanda kofu,

68. nati, 9 Utilote ife, Kristu Iwe; wakumenya Iwe ndani?

Mateyu 26