Mateyu 26:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onani, mmodzi wa iwo anali pamodzi ndi Yesu, anatansa dzanja lace, nasolola Iupanga lace, nakantha kapolo wa mkuru wa ansembe, nadula khutu lace.

Mateyu 26

Mateyu 26:42-56