Mateyu 26:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza kwa ophunzira, nawapeza iwo ali m'tulo, nanena kwa Petro, Nkutero kodi? simukhoza kucezera ndi Ine mphindi imodzi?

Mateyu 26

Mateyu 26:31-41