Mateyu 26:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwana wa munthu acokatu, monga kunalembedwa za Iye; koma tsoka ali nalo munthu amene Mwana wa munthu aperekedwa ndi iye! kukadakhala bwino kwa munthuyo ngati sakadabadwa.

Mateyu 26

Mateyu 26:17-26