Mateyu 26:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nati, Mufuna kundipatsa ciani, ndipo ine ndidzampereka Iye kwa inu? Ndipo iwo anamwerengera iye ndalama zasiliva makumi atatu.

Mateyu 26

Mateyu 26:6-22