Mateyu 25:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mfumuyo idzayankha nidzati kwa iwo, Indetu ndinena kwa inu, Cifukwa munacitira ici mmodzi wa abale anga, ngakhale ang'onong'ono awa, munandicitira ici Ine.

Mateyu 25

Mateyu 25:37-45