Mateyu 25:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Mfumuyo idzanena kwa iwo a ku dzanja lace lamanja, Idzani kuno inu odalitsika a Atate wanga, lowani mu Ufumu wokonzedwera kwa inu pa cikhazikiro cace ca dziko lapansi:

Mateyu 25

Mateyu 25:30-43