Mateyu 25:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mmodzi anampatsa ndalama za matalente zisanu, ndi wina ziwiri, ndi wina imodzi; kwa iwo onse monga nzeru zao; namuka iye.

Mateyu 25

Mateyu 25:7-23