Mateyu 24:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma 4 dziwani ici, kuti mwini nyumba akadadziwa nthawi yiti mbala ikudza, iye akadadikira, ndipo sakadalola kuti nyumba yace ibooledwe.

Mateyu 24

Mateyu 24:33-51