Mateyu 24:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye adzatumiza angelo ace ndi kulira kwakukuru kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ace ku mphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ace ena.

Mateyu 24

Mateyu 24:29-37