Mateyu 24:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pomwepo, atapita masauko a masiku awo, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwace, ndi nyenyezi zidzagwa kucokera kumwamba, ndi mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka:

Mateyu 24

Mateyu 24:24-34