Mateyu 23:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde, amanga akatundu olemera ndi osautsa ponyamula, nawasenza pa mapewa a anthu; koma iwo eni okha safuna kuwasuntha amenewo ndi cala cao.

Mateyu 23

Mateyu 23:1-13