Mateyu 23:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ha, Yerusalemu, Yerusalemu, amene umapha aneneri, ndi kuwaponya miyala iwo otumidwa kwa iwe! Ine ndinafuna kangati kusonkhanitsa pamodzi ana ako, inde monga thadzi lisonkhanitsa anapiye ace m'mapiko ace, koma inu simunafuna ai!

Mateyu 23

Mateyu 23:33-39