Mateyu 23:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka inu, alembi ndi Afarisi, onyenga! cifukwa mufanafana ndi manda opaka njereza, amene aonekera okoma kunja kwace, koma adzala m'katimo ndi mafupa a anthu akufa ndi zonyansa zonse.

Mateyu 23

Mateyu 23:25-35