Mateyu 23:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso, Amene ali yense akalumbira kuchula guwa la nsembe, palibe kanthu; koma amene akalumbira kuchula mtulo wa pamwamba pace wadzimangirira.

Mateyu 23

Mateyu 23:12-27