Mateyu 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka inu, alembi ndi Afarisi, onyenga! cifukwa mupitapita kunyanja ndi kumtunda kuyesa munthu mmodzi mtembenuki; ndipo m'mene akhala wotere, mumsandutsa mwana wa gehena woposa inu kawiri.

Mateyu 23

Mateyu 23:12-17