Mateyu 23:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsoka inu, alembi ndi Afarisi, onyenga! cifukwa mutsekera anthu Ufumu wa Kumwamba pamaso pao; pakuti inu nokha simulowamo, Ndipo muwaletsa amene alikulowa, kuti asalowemo. [

Mateyu 23

Mateyu 23:4-23