Mateyu 22:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ngati Davide amchula Iye Ambuye, ali mwana wace bwanji? Ndipo panalibe mmodzi anatha kumyankha mau.

Mateyu 22

Mateyu 22:36-46