Mateyu 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo anatumizanso akapolo ena, nanena, Uzani oitanidwawo, Onani, ndakonza phwando langa; ng'ombe zanga, ndi zonona ndinazipha, ndi zinthu zonse zapsya: idzani kuukwati.

Mateyu 22

Mateyu 22:1-11