Mateyu 22:38-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ili ndilo lamulo lalikuru ndi loyamba. Ndipo laciwiri lolingana nalo ndili, Uzikonda mnzako monga udzikonda iwe