Mateyu 22:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanena iwo, Ca Kaisara. Pomwepo Iye anati kwa iwo, Cifukwa cace patsani kwa Kaisara zace za Kaisara, ndi kwa Mulungu zace za Mulungu.

Mateyu 22

Mateyu 22:12-23