Mateyu 21:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo ananena kwa Iye, Adzaononga koipa oipawo, nadzapereka mundawo kwa olima ena, amene adzambwezera iye zipatso pa nyengo zace.

Mateyu 21

Mateyu 21:32-42