Mateyu 21:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mverani fanizo lina: Panali munthu, mwini banja, amene analima munda wamphesa, nauzunguniza linga, nakumba umo moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina.

Mateyu 21

Mateyu 21:23-39