Mateyu 21:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene Iye analowa m'Kacisi, ansembe akuru ndi akuru anthu anadza kwa Iye analikuphunzitsa, nanena, Mucita izi ndi ulamuliro wotani? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro wotere?

Mateyu 21

Mateyu 21:16-27