Mateyu 20:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onani, tikwera ku Yerusalemu; ndipo Mwana wa munthu adzaperekedwa kwa ansembe akuru ndi alembi, ndipo iwo adzamweruza kuti ayenera imfa,

Mateyu 20

Mateyu 20:14-22