Mateyu 20:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye anayankha, nati kwa mmodzi wa iwo, Mnzanga, sindikunyenga iwe; kodi iwe sunapangana ndi ine pa rupiya latheka limodzi?

Mateyu 20

Mateyu 20:11-16