Mateyu 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene oyamba anadza, analingalira kuti adzalandira kopambana, ndipo iwonso analandira onse rupiya latheka.

Mateyu 20

Mateyu 20:2-13