Mateyu 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pakumva iye kuti Arikelao anali mfumu ya Yudeya m'malo mwa atate wace Herode, anacita mantha kupita kumeneko; ndipo pamene anacenjezedwa ndi Mulungu m'kulota, anamuka nalowa ku dziko la Galileya,

Mateyu 2

Mateyu 2:15-23