Mateyu 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nakhalabe kumeneko kufikira atamwalira Herode; kuti cikacitidwe conenedwa ndi Ambuye mwa mneneri kuti,Ndinaitana Mwana wanga aturuke m'Aigupto.

Mateyu 2

Mateyu 2:7-21