Mateyu 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika ku nyumba anaona kamwanako ndi Mariya amace, ndipo anagwa pansi namgwadira Iye; namasula cuma cao, nampatsa Iye mitulo, ndiyo golidi ndi libano ndi mure.

Mateyu 2

Mateyu 2:4-18