Mateyu 19:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena naye, Ngati ufuna kukhala wangwiro, pita, kagulitse zomwe uli nazo, nupatse aumphawi, ndipo udzakhaia ndi cuma Kumwamba; ndipo ukadze kuno, unditsate.

Mateyu 19

Mateyu 19:11-23