Mateyu 19:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pali osabala, amene anabadwa otero m'mimba ya amao: ndipo pali osabala anawafula anthu; ndipo pali osabala amene anadzifula okha, cifukwa ca Ufumu wa Kumwamba. Amene angathe kulandira ici acilandire.

Mateyu 19

Mateyu 19:2-20