Mateyu 18:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati diso lako likukhumudwitsa, ulikolowole, nulitaye: nkwabwino kuti ulowe m'moyo ndi diso limodzi koposa kuponyedwa m'gehena wamoto, uli ndi maso awiri.

Mateyu 18

Mateyu 18:1-16