Mateyu 18:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma popeza iye anasowa kanthu kombwezera, mbuye wace analamulira kuti iye agulitsidwe, ndi mkazi wace ndi ana ace omwe, ndi zonse ali nazo, kuti akabwezedwe mangawawo.

Mateyu 18

Mateyu 18:15-28