Mateyu 18:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati mbale wako akucimwira iwe, pita, numlangize pa nokha iwe ndi iye; ngati akumvera iwe, wambweza mbale wako.

Mateyu 18

Mateyu 18:12-22