Mateyu 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga muyesa bwanji? ngati munthu ali nazo nkhosa makumi khumi, ndipo ikasokera imodzi ya izo, kodi saleka zija makumi asanu ndi anai mphambu manu ndi zinai, napita kumapiri, kukafuna yosokerayo?

Mateyu 18

Mateyu 18:9-17