Mateyu 18:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nthawi yomweyo ophunzira anadza kwa Yesu, nanena, Ndani kodi ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba?

2. Ndipo pamene Yesu anaitana kamwana, anakaimitsa pakati pao,

Mateyu 18