Mateyu 17:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye anabvomera, Apereka, Ndipo polowa iye m'nyumba, Yesu anatsogola kunena naye, nati, Simoni, uganiza bwanji? mafumu a dziko lapansi alandira msonkho kwa yani? kwa ana ao kodi, kapena kwa akunja?

Mateyu 17

Mateyu 17:19-27