Mateyu 17:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma ndinena kwa inu, kuti Eliya anadza kale, ndipo iwo sanamdziwa iye, koma anamcitira zonse zimene anazifuna iwo. Ndipo conconso Mwana wa munthu adzazunzidwa ndi iwo.

Mateyu 17

Mateyu 17:11-16