Mateyu 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa, Lero nkwa mphepo; popeza thambo liri la ceza codera. Mudziwa kuzindikira za pa nkhope ya thambo; koma zizindikiro za nyengo yin o, simungathe kuzindikira.

Mateyu 16

Mateyu 16:1-13