Mateyu 16:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anayankha iye, nati, Ndiwe wodala, Simoni Bar-Yona: pakuti thupi ndi mwazi sizinakuululira ici, koma Atate wanga wa Kumwamba.

Mateyu 16

Mateyu 16:13-23