Mateyu 16:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anati, Ena ati, Yohane Mbatizi; koma ena, Eliya; ndipo enanso Yeremiya, kapena mmodzi wa aneneri.

Mateyu 16

Mateyu 16:13-20