Mateyu 15:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Muli nayo mikate ingati? Ndipo iwo anati, Isanu ndi iwiri, ndi tinsomba pang'ono.

Mateyu 15

Mateyu 15:27-39