Mateyu 15:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Yesu anayankha, nati kwa iye, Mkaziwe, cikhulupiriro cako ndi cacikuru; cikhale kwa iwe monga momwe wafunira. Ndipo mwana wace anacira nthawi yomweyo.

Mateyu 15

Mateyu 15:23-36